Trending News:
  • Govt cracks down on illegal mining, warns of tough action
  • Ministry of Health surpasses polio vaccination target
  • Two netted for illegal possession of guns ahead of Easter
  • Zomba plants 2.4 million trees
  • Social workers push for new law to regulate profession
April 12, 2026
Yoneco FM
  • Breaking
  • News
    • National
    • International
    • Entertainment & Arts
    • Sports
    • Feature
    • Business
    • Health
    • Chichewa
  • Podcast
    • TIcheze
  • About us
  • Programmes
  • Our Team
  • Contact us
Search for:
  • Home
  • Chichewa
  • Page 2

Anthu ena ku Balaka akufuna bwanamkubwa achoke

February 11, 2025February 11, 2025 Smart SochelaChichewaNo Comment on Anthu ena ku Balaka akufuna bwanamkubwa achoke

Mzika zokhudzidwa zochokera m’mudzi mwa Ng’onga mfumu yayikulu Nsamala m’boma la Balaka, zakonza ziwonetsero za bata zomwe cholinga chake ndikukakamiza…

Read More

Mutharika akwiya ndi kumangidwa kwa mamembala a DPP

January 10, 2025February 3, 2025 Augustine MuwotchaChichewaNo Comment on Mutharika akwiya ndi kumangidwa kwa mamembala a DPP

Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Peter Mutharika ati ndi wokwiya ndi kumangidwa kwa posachedwapa kwa akuluakulu a…

Read More

CDEDI lati lipoti la ngozi ya ndege liperekedwe kwa a Malawi

December 18, 2024 Smart SochelaChichewaNo Comment on CDEDI lati lipoti la ngozi ya ndege liperekedwe kwa a Malawi

Bungwe la Center for Democracy and Economic Development Initiative (CDEDI) lati likufuna kuti zikalata za lipoti lokhudza za ngozi ya…

Read More

Chakwera walephera kulamulira dziko, watero Kabambe

November 28, 2024November 29, 2024 Augustine MuwotchaChichewaNo Comment on Chakwera walephera kulamulira dziko, watero Kabambe

Wolemba Lauryn M’banga Mtsogoleri wa chipani cha UTM a Dalitso Kabambe, ati mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera alephera…

Read More

CSAT yati iyamba kuphunzitsa anthu zokhudza nyumba ya malamulo

November 23, 2024November 26, 2024 Augustine MuwotchaChichewaNo Comment on CSAT yati iyamba kuphunzitsa anthu zokhudza nyumba ya malamulo

Bungwe la Centre for Social Accountability & Transparency (CSAT) lati kuyambira mwezi wa January chaka cha mawa lilimbikitsa ntchito yodziwitsa…

Read More

CDEDI yati ikukonza ziwonetsero zosakondwa ndi boma

November 19, 2024 Smart SochelaChichewaNo Comment on CDEDI yati ikukonza ziwonetsero zosakondwa ndi boma

Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), lati lachinayi likudzali lichititsa ziwonetsero mu nzinda wa Lilongwe zosonyeza…

Read More

Nthambi ya ndende ilimbikitsa ntchito za manja

November 9, 2024November 14, 2024 Alinafe NyasuluChichewaNo Comment on Nthambi ya ndende ilimbikitsa ntchito za manja

Nthambi ya ndende m’dziko muno yati kuphunzitsa anthu omwe akugwira ukaidi luso la ntchito za manja ndi njira imodzi yomwe…

Read More

Mkumano usonkhanitsa achinyamata 500 — NYCOM

November 8, 2024November 11, 2024 shadreck sindizaChichewaNo Comment on Mkumano usonkhanitsa achinyamata 500 — NYCOM

Bungwe la National Youth Council of Malawi (NYCOM) lati zonse zokhudza mkumano wawukulu wa achinyamata mdziko muno omwe uyambe lolemba…

Read More

CDEDI yati kalembera wa chisankho aime kaye

November 7, 2024 Smart SochelaChichewaNo Comment on CDEDI yati kalembera wa chisankho aime kaye

Bungwe la Centre for Democracy and Economic Initiatives (CDEDI) lapempha bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) kuti lisayambe gawo lachiwiri…

Read More

Boma ladzipereka pofuna kuthetsa njala

October 30, 2024November 1, 2024 Augustine MuwotchaChichewa / NationalNo Comment on Boma ladzipereka pofuna kuthetsa njala

Nduna yowona za malimidwe a Sam Kawale yati boma ladzipereka pofuna kuthetsa njala mdziko muno pogwiritsa ntchito ulimi wothilira. Iwo…

Read More

UDF sinalowe mu mgwirizano ndi chipani chilichonse

October 28, 2024October 29, 2024 Smart SochelaChichewaNo Comment on UDF sinalowe mu mgwirizano ndi chipani chilichonse

Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF), Atupele Muluzi, watsimikizira akuluakulu a chipanichi kuti palibe chipani chilichonse chomwe akukambirana…

Read More

Chakwera wakhazikitsa komiti yapadera yoti ifufuze za ngozi ya ndege

October 27, 2024October 29, 2024 Smart SochelaChichewaNo Comment on Chakwera wakhazikitsa komiti yapadera yoti ifufuze za ngozi ya ndege

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wakhazikitsa komiti yapadera yoti ifufuze zokhudza ngozi ya ndege yomwe inapha wachiwiri kwa…

Read More

Posts navigation

Previous 1 2 3 4 Next

STREAM LIVE ONLINE

report issues on gbv:call 5600!

report issues on gbv:call 5600!

Listen to YONECO FM

YONECO FM APP

The Equivalency Determination

trocaire

ISPCAN

Search

Search for:

National Child Helpline call 116

National Child Helpline call 116

subscribe for our breaking news

Loading

Follow Us!

Follow Us on FacebookFollow Us on TwitterFollow Us on MySpaceFollow Us on Blogger

Download the Helpline App

LikeBox

Copyright © All rights reserved.